Email a copy of 'Super League of Malawi clarifies on relegation of teams' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Super League of Malawi clarifies on relegation of teams' to a friend
Mighty Be Forward Wanderers goalkeeper Richard Chipuwa is facing a lengthy spell on the sidelines after sustaining a groin injury...
koma munthu ot amadya nsima ndi ndiwo akhoza kumalingalira kut noma nkuchitidwa relegate?malingaliro menewa ndi munthu wochokera kuntaya cheeeeeeee
Amaopetsa noma, chikhala kuti nyerere zinakakamirabe ku relegation zone bwezi akuti atuluka awiri. Koma popeza nyerere zasuthako ku relegation zone basi plan changed
Mzuzu ikukuladi eti mpaka ikhonza kupanga host 3 Super League teams? Hahaha ma fixture nde avutatu because kumpoto kumaenera kupitidwa kamodzi ndekuti for instance Bullets ikapita ku North iziyamba kusewera Friday, Saturday ndi Sunday!! Shaa after game uzimwedwa and sampling paParis Club Friday and Saturday.
Why 16 team? That is promoting ineficiency.
Good idea. You don’t change rules midway a season
Mwatipusitsa
Mateam a zigawo abwere mu super league koma ochoka muchotse awiri, ndiyeuyu wapulumuka ukuyu asanyadire kuti zake zayeda ayi ,pakhale ma play off ndi ma second team a zigawo aja.Mukatero ndiye kuti team number 16 yapezeka.
Nkhanga zaona. Mumafuna kupulumutsa Fisd koma zakanika. Mwaona zoti sizitheka chifukwa choti ili pansi penipeni. Makokeredwe akanika pamenepa. Mbuzi za Sulom.
U should make it 20 not 16 and harmonise the calender with other international leagues like epl,so that when our friends are off season we should also be off season,including the transfer calender.
Osangoyamba Season ino bwanji?