Email a copy of 'Thindwa joins Mighty Wanderers on loan from Zimbabwe’s Caps' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Thindwa joins Mighty Wanderers on loan from Zimbabwe’s Caps' to a friend
Democratic Front(UDF) National youth Director, Ibrahim Maloni, has become the latest statistic of the gun crime in the country after...
Akanasankha timu yomwe umasapota ukanati chani??? Nsanje a Malawi muzasiya liti.tiona ngati sakuchinyani pagolo panupo.
Iwe ngati zakupweteka pita ukagone,tikunena za thindwa going ku wanderers not ku bullets, let NOMA fans comment on this.
Ngati ali mtop form yazigoli bwanji Samamulowesa ku cups?
Azibwerabwera ma Strikers amenewo.
Mike ukubwera bho,unayamba wakoza kapasi kut kamwamba katsike.can u see nw ma player akofuna noma basi,nothing else,asuuuuu azipita.tchito sanagwire afuna ndalama hw?
lacking game time?Did I hear properly?ndiye muziti he is a profolic striker ?kale komwe kaja not now watha uyu,mudzandivomereza.
timu yayikulu izidziwika ndiosewera akeso.
Did i hear u mr butao saying Thndwa iz always on top of his gem? Fallacy
Vuto ndiloti zikakhalapo(ndalama) a Malawi sitizigwiritsa bwino ntchito. Mukuti ma striker 11 mtimu yimodzi? Vyachani vyonsevo? A Coach talongosolani.
Too many cooks spoil the ….., mwawononga team inu kodi coach bwanji mukungotenga mapuleya ambirimbiri? Mu Malawi siziphula kanthu zimenezo! A bad carpenter blames his tools(strikers) always. A Technical Director zoona mpaka mastriker 11 mutimu?