Email a copy of 'UK-based Malawians to launch Secca charity at dinner dance: To help orphans, widows' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'UK-based Malawians to launch Secca charity at dinner dance: To help orphans, widows' to a friend
Red Lions Football Club, the oldest Malawi Defence Force top league outfit have sacked coach Mike Kumange and his assistant...
Mafuno abwino SECCA-UK. Pitirizani kuthandidza ana amasiye, nkhalamba ndi ena osowa. Anthu amene SECCA yakhala ikuthandiza kuno ku Malawi ndiyotamandika. Ana amasiye ambiri mumawadyetsa chakudya chabwino, ambiri adamaliza masukulu ena mpaka kupita ku ma college. Nkhalamba mumadziveka zobvala zabwino, komanso mumasamalira nyumba zawo. Ambiri mumawathandidza nthawi ya njala ndi chakudya. Mulungu adalitse nonse.
Why would you have board members from the same family? Husband, wife and wife’s aunt, is this a family affair or a charity organisation? Smh 🤔🤔
A Njazi palibe za family affair apa. Anthuwa ndi odzipeleka kuthandiza anthu osowa mwaulele. Ngati inu muli ndi zokuyeneretsani, bwerani mudzathandidze nawo ntchitoyi.
Tamva khalani pansi.
Ma board member onse ogwira Ku NHS and related organisation? Okhe mukatenganenso ndi anzanu a Ku NHS mukadye Ku Cedar Hotel kwanu kwausiluko. Ma hotel onse ali mu BD1 ndati azikapita Ku M62 za ziii. It seems you ahve already lost touch