Email a copy of 'Wanderers losing their marbles, ‘Neba’ calls for inquest' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers losing their marbles, ‘Neba’ calls for inquest' to a friend
Football Association of Malawi (Fam) is investigating suspected gate ticketing fraud in which K5 million shortfall has raised suspicion on Saturday’s...
system yakamenyetsedwe kumenyetsa striker mmodzi pali mzeru mukupanga defend chani? rubbish yokhayokha imeneyi
employ kinna phiri. mabvuto atha. he is the best coach available
solution:ma player onse amene tilinawo ngongole alipidwe or azipita,ma player aja amati akuchoka…and ife tinati ndi masenior player asapite..amene aja azipita chifukwa amakhala ngati ndiolimbikira koma amakhala akupanga sabotage team pokhumudwitsa azizawo cholinga management kuphatikizapo captain yilipoyi ioneke yosatha.