Silver plot Bullets raid when transfer window opens

Silver Strikers  are hoping to bolster their squad with the double signing of champions Big Bullets pair rejuvenated striker Chiukepo Msowoya and midfielder Dalitso Sailesi.

Dalitso Sailesi: Targeted by Silver

Dalitso Sailesi: Targeted by Silver

The Bankers have set their sights on the two players and Silver’s acting general secretary Fred Kalonga confirmed the development saying when transfer window opens, they will launch the bid to sign the players.

“Indeed the supporters came to us requesting the committee to bet on board these two players. But we told them that as a committee we are yet to decide on that,” Kalonga said.

The development comes in the wake of allegations that Victor Limbani is intending to return to Bullets.

“However we are still going to sign some players during the mid season break. We need a goalkeeper, a defending and attacking midfielders,” he said.

Bullets Vice-General Secretary Kevin Moyo said he was aware of Silver’s intention to entice their players.

“We are aware of their interest but there’s nothing official about this. There is also no player request,” Moyo said.

“But we are not letting our players go and we are also doing well and I don’t think the players would want to leave now players,” he added.

The banker are now keen on reinforcing their squad with more players  hile Bullets who are keen to defend the title would not let their key star leave.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Please share this Article if you like Email This Post Email This Post

More From the World

43 thoughts on “Silver plot Bullets raid when transfer window opens”

 1. mwaxy says:

  tisiyeni ma wule. yanjiru siswa mazira osamaiwala. anzanu zikamayenda inu chimtima kuunooo kuwawidwa! sizitheka mukufunazo.

 2. EPHRAIM JB says:

  INU AKELVIN MOYO AUZENI ASLIVA TISAYAMBANE.ASOWA KOSEWERA ET.NGATI NDALAMA NANUSO MUNYA.ZOT NDALAMA TAYAMBAKO KUTAPILA KU SUPALIG MWAIWALA?TAYELEKEZANI TKUMATCHANI.

 3. Wa Maule weniweni says:

  Silver inafika poti ngakhale kukatenga Messi ndi Hazard sangawinebe chifukwa vuto sima player but the kind of treatment subjected to players. Apart from money, players need to be treated like human beings and not as you do with a toilet tissue. Take them both for a while but they will soon return to where they belong (BB) after eating your money for no benefit at all.

 4. Prescott says:

  A Silver Mitu ngati a Sakhwi, Chaka chatha munachita chimodzimodzi kutitengera ma players athu, koma simunawine Ligi. Bwanji simuyang’anako ku matimu ena. Kukula mitu sikudziwa ku heda mipira. Miyendo ya mateweyo mungaserere mpira agalu inu, mutisiyire ma players athu. Yerekezani kuwatenga awiriwa tikusweninso kachiwiri. Kumbukirani kuti potsegulira ligi tinakukhomerani pakhomo panu, mukabwera ku Blantyre tidzakhoma nsomali womaliza.

 5. Nkhuku ya njiru siiswa mazira, Sailesi mwamudziwa liti kuti ndiwabwino, nanga Chiukepo simumamuona nthawi yonseyi? Munyanya matama lero ndiye mwasmwa mtengo wogwira apa, mapuleya athu siwogulitsaaaaaaa!

 6. Zachisoni Phiri says:

  The MENTIONED two are not good players SILVER GO TO CHIPIKU LEAGUE and get good boys not nyangwitazi

 7. Zikwanje Mukangoyerekeza says:

  Mukangoyerekeza kukhala mugulu logula Chiukepo ndi Dalitso,mudzafa imfa yowawa mabankazi.Mapalestina adzakunyenyanyenyani ndikukuphwanya ka coaster kanuko kanuko.Mukusewera ndi masapota olusa a Bullets.Muzafa imfa yowawa.

 8. Richie Zulu says:

  Misala imeneyi yokha a Silver simuchila basi. Kugulila nkhwidzi zotsatila zake ndi number muliyo. Msowoya & Sailesi not for sale.

 9. MAPWEVUPWEVU says:

  NYANI WAKHOTA MCHIRA BASI AKULUAKULU A SILVER MITU SIKUYENDA MUKATENGE MSOWOYA ZOONA

 10. mchenga patrick says:

  Chomwe a silver mungapange muwapatse a BB osewela anu akawakoze azipanga traning ndi BB muona kuti ziyenda

 11. Jamy says:

  PALIBE PLAYER WAMALONDA KU BULLETS NGATI NDALAMA ZAKUCHULUKIRANI GULANI MANKHWALA MUKAPEREKE KU CHIPATALA. SILVER YACHITA MISALA YASOWA CHOCHITA YACHITA CHILOPE BASI. PAJA MUMATCHUKA NDI MATAMA MUNYA MUONA CHIUKEPO NDI SAILESI NOT FOR SALE PITANI MUKAKOLOPE NYANJA.

  1. Beloved says:

   Imeneyo ndiye timati nsanje awiri munatenga aja mukulephera kuwagwiritsa ntchito ndiye mutengenso ena ai apa ndiye sitilola ngati a silver muli nazo zochuluka kaguleni ku jubeki aliko ambiri.

 12. TENDA K says:

  BASI ASILVER MWATHA.

 13. Kenneth duwa says:

  Amoyo pamodz nd mwamad ndisava zmenezo.Tiyeni titole chikwama chamu Roma,tiwine super league,carsberg nd standard bank kuzera maplayer ake omwewa monga mwaiwo
  chiukepo,
  sailes nd ambiri.team ya banker yophera tsogolo player. mukudziwa

 14. Mzambia says:

  ngati zachulukira ndalama agule coach wabwino.kapena azichindira mahule mubwandilomo.zotionongera maplayer athu ife nyasi zimenezo ayi,haaaa!!!!

 15. Shekman says:

  Nyansi Zimenezo Ife Ma Banka Sitingatenge Chiu Oguga Kale, Alipo Ma Player Omwe Tigule Osati Awa Idzi Ndi Dzanu Mudzimaliza Nokha, Koma Tikangoloza Player Talozatu Paja Angakane Kubwela Ku Capital Ndani Kumakakamilako Chani Ku Kabula Inaguga BT ( PANO NDI HOZA CASHGATE) Dzichakachikani Ku Btown Kwanuko Mudzizisova Tithyola Mpanda

 16. murray msowoya says:

  Mukamva kuti ntopola nde umenewu. Is it BB that has got players for Silver? Anyway, ubwino wake ndi oti amakatithandiza kuchinya Silver’yo.

  No player from BB, of late, joining SS has been a force to be afraid of.

  Amakangothelako

 17. wit waBB says:

  hahahaha where z pindani,vibrey and tizyo kumeneko ndikothela ma player

 18. Hardson says:

  Timakamba nthawi zonse kuti Bullets imasewera ngati team not as an individual. Atengeni mukawathenso mmene mwaathera achina Vbri suyo Vibri akufuna kubwerera ku Bullets. Kumakhalako ndi manyazi please.

 19. phwethulani says:

  moyo usayerekeze ndi azizakowo zoti Anyamata amenewa achoke.Zotiyamba ife ayi.

 20. Adam christon Masamba says:

  Inu anthu; amene mukutsogolera team ya silver striker, makamaka kapena chenicheni mukufuna chiyani ku team yathu ya Big Bullets? Mukufuna kuti, team yathu ya Big Bullets ithe? Mukukumbukira chipongwe chomwe munatipanga nthawi ija; munatilanda maplayers omwe tikadalira, panthawi yomwe tinali m’caf. V @ T, munawachosa mwachipongwe, pamene tsogolo lawo linali ku bullets kuja. Lero, mwayima pachulu ndikumakweza mawu oti mukufuna Msowoya ndi Dalitso, ndizokuyenelezani zimenezi, inu anthu asilver?

 21. mulupa;e says:

  Let these guys to join Silver so that they should be trained skills for scoring into their nets.

 22. nyerere says:

  Neba asiye a Silver agule mapuleya amene akufuna. Ndipo ndi nthawi yoti chiukepo ndi Sailesi atole chikwama.

 23. humphreys says:

  Sorry ma bankers,u wil never break the peoples team even if u sign the whole team bullets wil remain the champions for ever,lol

 24. phiriwaphiri says:

  hi, a free advice to all those who would like to leave BB,ku silver kumakhala kothela, do you remember that left back from SILVER WHO CAME B.UNITED, ANANGOMULODZA BASI FWA, LOOK AT NDAZIONA CHATSALIRA THE SO CALLED 6 MILLION, HE NO LONGER WORTHY 6 MILLION, 250,000 MWINA SO IF YOU WANT TO GO TO SILVER, GO, BUT REMEMBER WILL NEVER DIE, WINA NDI UYU AKUFUNA KUBWERELA WHAT HAS HE SEEN THERE,?
  TO YOU MWANA WA KWITHU CHIUKEPO, WHEN THE MOZAMBICAN SIDE DUMPED YOU BB PICKED YOU AND WASHED YOU SO IF YOU WANT TO GO GO, BUT YOU WILL REMEMBER THESE WORDS WA KWITHU

 25. Totolitotoli says:

  Thoughts of idiots,Silver forced Victor and Tigzobere into their team but what came out of it,’Maganizo auchewa olanda akazi achainiake akagulitsa fodya ndi omwe uli ku Silver’.Buying quality players from Bullets it’s not the answer to your dismal perfomance but rather poor administration of the club.Get willing players to play for your team like those in your reserve side but these other players will let you down.You can force a horse to the river but you can not force it to drink.For Victor go where you belong.Silver is full of idiots whose IQ needs to be examined.

 26. ZZ Junior says:

  Silver dare try to do that. you will meet the wrath of mapalestina and those players akamenya mpira kumwamba ndithu.

 27. victor gama says:

  Akuguleni basi mulibe ndalama mwina mupezeko yonyenyeka.

 28. kanyimbi says:

  Silver yawonjeza. This team is full of envy remember it refused to loan players to BB during their CAF campaign. So what Bullets should do is to sell these players at 1 Billion Malawi Kwacha and we will see if they can pay. If they will pay then Bullets will be a wealthy team. Kulanga ntchentche ndi kunyela m’madzi.

 29. Longa Mbuya says:

  Silver took Tizgobere from Bullets now Tizgowere akumvekapo apa? Amene atapite akathera konko asiyeni. A Chiukepo anafika pokutha koma thanks to Bullets the guy is back. My oinion.

 30. Massa says:

  Koma abale a silver amationelera bwanji chifukwa choti ali ndi ndalama ai zisatero ndipo inu a technical yathu musayelekeze

 31. bbsupporter says:

  Silver is a team full of fools.

 32. Anzwaa'73 says:

  What’s the use of having Silver Reserve when all you do is buy players from other clubs?

 33. Phwexy says:

  Sitilola zimenezo.. Na BB ndi game yobwenzera zija za mu caf zija musaiwale a silver..

 34. silence Binali says:

  Chiukepo &Dalitso are not for sell,kumeneko ndikuwaputa dala mapallestina,I’ve tinasiya ndeubbut if provoked we will defend ourselves

 35. Paul Omaliza Makoka says:

  A Silver Ndinu Opepera & Opanda Nzeru. Mwaiwala Munatikaniza Ma Player Anu Tikukonzekera Caf? Iyi Ndi Nkhondo Mukuiputayi. Kupusa

 36. LIZULU says:

  MUKUFUNA KUMAONONGA MA PLAYER ATHU NGATI MATIMU A JONI BWANJI?TIZGO NDI LIMBANI MWAPHA PANO MUPHENSO CHIUKEPO NDI SAILESI?KONZANI MA COACH ANU SADZIWA KUPANGA DEVELOP MA PLAYER AMANGODZIWA KULOZA OTI ASEWERE GAME BASI.MA PLAYER ANU OMWEWO ATABWERA KU BULLETS MUKHOZA KUWASILIRANSO.YOU HAVE GOOD STRIKERS HARAWA CHISAMBI TIZGO LIMBANI CHATSALIRA BUT POOR TECHNICAL TIPATSENI TEAM TIKOCHE IFE!!!!!!!!!!

 37. Ndiye ufitiwo chifukwa tilibe sponsa

 38. titus Scoti says:

  Ndipo inu a Silver musayesere dala enticing the duo. Pitani ku EPAC or Fisidi Wizards mukagule anyamata. Kumeneko you will find willing sellers!

 39. captain says:

  Mmalo moti mukatenge a china messi Kunja uku. Salary pa Chaka ngati budget ya ministry of education yonse

 40. Ndiye ufitiwo chifukwatilibe sponsa

 41. phaka says:

  Chiukepo???why buying ove age player…..

 42. VD says:

  Mabanker musovaaaa! Mukatenge maplayer ku reserve yanu.

Comments are closed.

More From Nyasatimes