Head teacher sexually assault 14-year-old pupil in Mangochi
Chilipa Police Unit in Mangochi is keeping in custody a head teacher of Kapire Primary School for being suspected of defiling a 14-year-old girl (name concealed) who was in standard seven at the school in the district.
Mangochi police publicist Rodrick Maida confirmed the arrest and identified the suspect as Gnazio Goliati of 55 years of age.
According to Maida the suspect was on 17th October 2014 while his wife had left the house, asked the girl (victim) to go to his house and prepare him lunch and this gave him an advantage to defile her.
“It seems Goliati used force to defile the child to slake his libido because the victim’s under wear (pant and peat coat) were torn apart,” said the police publicist.
“After this happened, the girl did not disclose the ordeal to anyone until she was quizzed by her parents when they noticed that she was pregnant,” he disclosed.
The district’s police spokesperson further added that rumours speculated like bush within the girl’s compound and these force members of the general public to tip Chilipa Police on the same which led to the arrest of the culprit on March 13th2015.
The head teacher will appear in court soon where he will answer an offence defilement which is contrary to section 139 of the Penal Code.
Goliati hails from Mbedza Village in the area of Traditional Authority (T/A) Nazombe in Phalombe .
Follow and Subscribe Nyasa TV :
55yrs-14Yyrs….Mmmmh,Yalakwa.
more fire south
Ana a chawa kudelera paja amati mwamuna samapha
wnawonso ayawo ndi achina amberechile kumtumbo kwangali ngöngole mwina kanatenga mapensulo wa ahead?
Tiziti Azibambo ozerezeka ndi chigololo ali kumwera eti?zamanyazitu izi abale.ena timagalimoto tawo,kumachita kuika ka tintedi chifukwa chokuti atonyamula kamwana ka saizi ya mwanawo,kumanamizira kuti akayesa mwanawo sanapite ku sukulu,kuli kufuna kupweteka mwana wa nzawo.
Taganizirani ali wanu mwana,atatengana ndi mchidala ngati inu bwaa? akulirenji bvumbwe otsakamira pa ka tsekera kang’onong’ono.kuti muone zambiri amalawi anzanga,muzitchera pa lanchi,enanu mudzakhumudwa.akunamiza anchito pakhomo kuti mzake wa mwana wanga.timatoyaluka ife amene timatoziona ndi maso.
Tiziti Azibambo ozerezeka ndi chigololo ali kumwera eti?zamanyazitu izi abale.ena timagalimoto tawo,kumachita kuika ka tintedi chifukwa chokuti atonyamula kamwana ka saizi ya mwanawo,kumanamizira kuti akayesa mwanawo sanapite ku sukulu,kuli kufuna kupweteka mwana wa nzawo.
Taganizirani ali wanu mwana,atatengana ndi mchidala ngati inu bwaa? akulirenji bvumbwe otsakamira pa ka tsekera kang’onong’ono.kuti muone zambiri amalawi anzanga,muzitchera pa lanchi,enanu mudzakhumudwa.akunamiza anchito pakhomo kuti mzake wa mwana wanga.timatoyaluka ife amene timatozina ndi maso.
Boko Haram yonseyi mpaka kamwana kakang’ono.kodi azibambo oterewa sachita manyazi,akamavurila tiana ta saizi ya ana awo?
Ambuye nthawi yatha bwerani mudzaweluze dzikoli
Peat coat ndi chaninso abale? It’s “petticoat”
WAONJEZA WAKOZERA TIKITI
Chegoliati Mwatichitisa Manyazi 55-14=41 Ahead Autsiru
Nanga Aphinzitsi Anu Muwalangiza Kuti Chani?
people do on 2 others wat u wnt them 2 do 2 u,wat if she ws ur daughter?
Koma Azathu akumwera mwanyanya ndi nkhani za zigololo, mukukhala ngati odziwa kwambiri kuchindana ndinu nokha bwanji? Daily nkhani zachiwerewere ndizakumwera, ayi. Ndiye chifukwa chake dzikoli lingofunika tigawanepo apa. Mumatipangitsa manyazi
Alomwe ndi ntundu wa zonse mommo.Chilichonse amatha.Mitundu inayi ndimbudzi zogona.Kuba,kuchindana,kulamula dziko………zonsezi ndi za alomwe.
Koma ALOMWEEE kukonda kuchinda.
Alomwe inu koma muzamva inu
Wadadz mkamwa iwe, tsitsi lidzamera mkamwa mwakomo ukadzasya kulimbana ndi alomwe! Too much over generalisation, kungot anu samaonekera nde muli ndundu ngat zanu zli bwino, chikhala kut ukachita choipa umafa pomwepo bwedz iwe kulibe
There r so many teachers who dat to innocent girls. Awamange mbambo ndihule kwabasi siyekhayo mwana.
What iz going on,mahule otchipa onsewa?
Can’t these sex perverts learn to respect children and tangle with willing adults?
Aaaa koma headteacher uyu anakhala chisiru ndithu ifetu amatenga mahule khara kongolanso kambiri koma kamwana ako aaaaa…. Mache anali kutieeeee
peat coat instead of petticoat, koma ya!
assault or defilement? And how does torn underwear show systematic defilement? Give us facts please!
Anayamba kalekale ameneyu,ndimkhalidwe wake.apandibwe basi.
uku ndi ku balaka guyz.mangochi kulibe kapile.inu aku balaka mukuzolowera ndi illuminat.komanso mukut zamkat znang’ambka komanso mwanayo mpaka mimba?timve zit.apandidwe bas!!!!.mwana wamzako ndiwako yemwe.nxt time azibambo oterowa azlangidwa ndi achinyamata not kuboma.i thnk tingachepetse chizolowezi chotere.
Shame. I know this dude. He was teaching at nasolo at mpale and this was his brhaviour kungoti ayawo amamubisa. He even told me of his transfer and I told him to stop his behaviour. His current wife anamupeza mu njira yomweyi. Anali wantchito then malyolyolyo mpaka mimba nkazi woyambayo ndikuyituluka. Shame
A story from my school shame the headmaster
Kukhala ndi zaka 55 nde kut ali ndi chachikulu ayi,kma nanuso anthu mukamaika ma comment muziganizila,mwanao chinamupangitsa kut apiteko yekha ndi chani ku nyumba ya mu heads,ndipo atamaliza kumupunga bwanj sanauze aliyese,part ongambika pa 14 kufikila tsiku la lero pangakhale kut amamusunga patipo part wake ongambikayo? Ndipo pali mafuso ambiri pamenepa oasangot pot alomwe ndi opanda nzeru ayi
Changu 14 years ameneyo, Nanunso ana aschool apano, ma skirt talikitsaniko ndinawanva akunena kuti ”Salafinna style”, akuti tylor asoke kakafupi kungowelama zonse ma Offals kuoneka nangasi aphuzitsi amati can u rub the Bold eh, makolo mwana asanvale skirt yaifupi wakuschool ayi, asanvale ngati Hule mwana ayi, ma Min Skirt ndiama Hule amatitsatsa Bussiness osati mwana omwa ink ayi, kutukuka sikunvula ayi, umenewo ndi umbuli, ndiye akuchindani Heavy faz idatopa ndi chilungamoooooo!
Lolani tiwana tidze kwa ine,pakuti ufumu wa kumwamba uli wawo.Tsoka kwa iye ochimwitsa mmodzi mwa ana awa.Kukanakhala bwino kuti chimwala cha mphero chimangidwe nkhosi mwake,ndikuponyedwa pakati pa nyanja.
koma alomwe sizinthu kupha ma albino nokha,chigololo mugalimoto alomwe,defilement alomwe,uhule,kuba alomwe nditonama ngati?
Ndi alhomwe ntchito yawo yokonda zachigololo basi, masiku apitawa tinamva za alhomwe kuchita zachisembwele m’galimoto pano lhomwe wina kumangochi.
Headmaster ndiwe mfiti
A std 7 girl too young 4 a granpa like u shame on u, ngati simukudziwa akulu mwaononga ndi tsogolo la ana anuomwe so its time u reap what u sow
Soap ina imangokula ameneyu wayenera kukhala mfiti osamagona ndi ana ake bwanji because 55 years ana ake are more than 14 yrs. Education minisry munapereka u head kwa phycratric patient mumaopa kolodzedwa uyutu ofunika castration basi.
Mugabe 90 years mkazi wake 49…. Size ya bo nawonso anayambira pompa
koma iwe headteacher ndiwe mbudzi yeniyeni. mahule onsewa sunawaone mpakana kuphadzula kamwana? ndiwe gulugufe wopanda nzeru.
Comment; amafuna bele nganganga amwene,ha ha ha.
alomwe,alomwe nophiya
that’s very bad
Alomwe
Ku xalima kwa khombeza, matenje zone, mphuzitsi anagwidwa ndi mwana wa 8 usiku mu staff room akugonana.
simwana uyu bwanji xamaulura kwamakolo ake or kwa anzake?what kind of a child 2 kip secret de way she dd?chinali chizolowezi kudyanako amenewa
Zochitisa manyazi
Osamasekerera mbuzi zikamapanga zopusa chifukwa ndikuononga kumeneku
Comment osamanyengerera makolo pogwiritsa ntchito phala bwanji anzao2 akufewa ndi amai a eni mpaka2 kumaliza mudzi onse, koma mahead muyaluka2 kukhala ife mukanamati ndi ana angoyamba kumene ntchito kkkkkkk obadwa kale amuona fisi mochedwa2, eeiiish asova ameneyo
Alomwe opanda nzeru
.Mukamathamangitsidwa kumeneko mudziti anthu aku Mangochi ndi oipa. Mchira osavinidwawo osamakwera alomwe okokedwa amzakowo bwa?
Comment,nkhaza zazikulu zedi,munthu wa zaka 55 kukagona ndi mwana wa 14yrs.Boma lichitepo kanthu apa ndithu