Follow us in Twitter

10 replies on “hhhh”

  1. Asaaaaaa. A Thodi ndalama mmanyengera a zimai a eni ake zija ndizakuba??? A Mary aja amafera ndalama as eni ake????? Daaaaamn

  2. The conviction alone is an enough one way ticket out of civil service… For morality and integrity sake, we cannot have a country’s national intelligence chief being a fraud convict; this is moral turpitude of the highest order.

  3. Mbava… Tsopano munthu ngati uyu nkumakhala pa helm ya chitetezo cha dziko a Chasowa akhala angati? Eish!!!Koma boma ili. Ambuye tikhululukureni….A Navicha koma Chitetezo chanu ndi chokwanir”? Tisamve zoti mwasowatu. Munthu woophyatu uyu.

  4. a thodi mumafuna kumuomba mzimayi bwezani ndalamazo bwanji ndalama sizimakukwanani mwadya zambili ku immigration pano mwati mumufwambe navicha shaaa mwayaluka

  5. Mr president
    Is this type of people you give responsibility? Just like Dr ntaba.
    Please do not ask me!!! Ask the court.
    Have a good day sir

Comments are closed.