ANTHU 26,000 ALI NDI KACHILOMBO KA HIV KU NSANJE

Kafukufuku wa kufala kwa kachirombo ka HIV yemwe bungwe la MACRO linachita mb’oma la Nsanje, waonetsa kuti pali kukwera kwa chiwerengero cha anthu omwe atenga kachiromboka kuyambira mwezi July 2022 kufikira July 2023.
Bungweli latinso matenda opatsirana pogonana akupitilira kukwera mb’omali.
Ndipo pofuna kuthetsa vutoli bungwe la AlDS Health Foundation lakhala likupereka ma kondomu oposa 500, 000.
Pakadali pano, anthu pafupifupi 26,000 ndi omwe ali ndi kachirombo ka HIV m’bomali.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Sharing is caring!

Follow us in Twitter
Read previous post:
Forest Guard severely injured at Chikala in Machinga after confronting charcoal burners

One forest guard from Chikala in Machinga has been severely injured after being cut on his left cheek with a...

Close