Mwanache denigrates Tay Grin over Malawi Music Awards
Hip-Hop is competitive art form; emcees going back and forth on a beat and not on social media.


All that work is shown through accolades but last year’s Music Malawi (MUMA) awards left a lot to be desired, according to some fans and artists.
Well, Prime Time Media artist Mwanache hasn’t let go yet and had some words directed towards Best Hip-Hop/Rap award recipient Tay Grin this week.
Looks like Mwanache, whose hit song “Zimandukhudza” with legendary Lulu has been dominating charts and airplay, is feeling he’s going to get robbed at the next MUMAs or he’s just threatened with competition? You decide.
Tay Grin has not put out any new music lately after the award-winning “The Beach” feat. The Very Best and Seye as well as “Beautiful Girl” with Afro RnB maestro Maskal.
Read Mwanache’s Chichewa open letter to Tay, which was posted on Facebook but was later deleted:
“Dear Limbani Kalilani AKA Tay Grin kapenanso kuti Nyau King,
Waona mmene mamemba akuvutikira apakuphika nyimbo pa Malawipa eti? Daily mu studio kuweka harder. Nde Chonde, sizomati chaka chikamatha mungobwera nkumenya ka single then video, then akuti nkudzawina AWARD,. sibho chonchoman, kukhala samatero tonse ndi aMalawi.Komansotu mwina ulendo uno olo mutangokhala phee! timvanso kuti mwawina ndinu, kukhala samatero man. Anzanu one to thirty, jan to dec…pamene inu kamodzi kenkeni. Ngati mufuna tiyambile limodzi liwiroli mukamadzawinatizidzati mpake osati kuvencha tamvana eti????
Ndatha ine Limbani nzakonso koma Mulolo.#zikomo”.
kkkkkkkkkkkkk tay grin ndi more….
Guyz tisamangoona pafupid zomwe akunena mwanache sizabodza .limban kalilan or atat asayimbe athabe kuwina guyz ndiye sizabood zimenez…..
money talks bro….mwanche
mwanache ndi mbola!! bizy hating why!!
pepani amwene mwina munalemba mutaledzera ntonjani!!!
kkkkkkkkkkk
PRIMITIVE GENERATION
Zamkutu. Iweyo or swag ungafanane ndi Tay Grin? He won a BEFTA award in UK beating some African Heavy weights in Music, Ndiye iwe ndi kandani? The collabo of the Very Best and Seye proved that Tay Grin knows his game. His targeted audience is not only Malawi, but the whole world. Koma inu music kumenya zoti tizimvera mu Ntandiremu, Kwa Chinsapo kokha kuno, ndiye muziti muwina? Ng’oooooooo!!! Grow up kid. Besides u have just shown that your level of intelligence is low, hence u will not win any award till you change your thinking and work harder than before.
Mwanache ua bizy hating the master of the game iweyo? Kkkkkkkkk…ukulira ndi ma award a local pomwe mzako amawina ma international awards oti Inu ndi phala lanu lija simungawine olo xitaphweka mpaka…..dnt b a hater but learn from the best
Mwanache ua bizy hating the master of the game iweyo? Kkkkkkkkk…ukulira ndi ma award a local pomwe mzako amawina ma international awards oti Inu ndi phalanx lanu
kulimbana ndi tay grin ur just wasting ur time, sungafanane naye, awanso ndi ndan kodi? akufuna potchukirapo chan?
100 songs but same style = 0 awards
kulimbana ndi inkosi grin ndikutaya thawi uzachedwa ase grin ndi more
Tay Grin may not be the most gifted rapper in the land, but he knows his game. And for all he does, he deserves the bling, coz he the best. Some of you just need to grow up, and learn that its about volumes but quality. #luzers
za ziiiiiiii
awaaa akulila zopanda mutu…am sure if u had the same chance to record one song a year and win an award u wud do the same…bwana its about working smarter not harder…inu mukulimbana ndi kukumba dzenje pamene anzanu apeza machine okumbila…stupid guy…ulila choncho…and i dont even like tay grin or his music…
These days u need to work smarter not harder…
Pali nzeru spa? Timvepo Chani tsono. You can work harder 1-30 as you rightly put, but if your work is trash you don’t expect to win. Inuyo zipangani zanu and prepare thoroughly at the end of the day its people who vote and mind you,! They don’t look at how long you took to come up with that thing but rather quality. Personal attacks is a sign of immaturity and ubulutu as well as KUSATHA. concentrate on your things.
It’s not just a matter of spending the whole year in the studio…each month!!But good,substantial music matters.Quality of your music also matters as well.
GUYS! DO NOT BE BACKWARD, THESE ARE COPYCATS, HIP-HOP IS COMPETATIVE ART FORM IN USA NOT IN NYASALAND, AWA NDI MANIGGA ANJALA, JOB OF THE SCHOOL DROPOUTS.
Finally the truth!
Life is not fair my friend. Cash rules everything around. Credit is not given where it’s due.
nonsesnse
ngati nzako amatha ntchito yake usamude. tay grin is an artist on another level my friend, recognised internationally.
you should also understand that in marketing, you have to strategise your album release dates so that the public doesn’t get tired of your music quickly.
makape ena amapanga release an album every year. ena ali cha m’ma kuyimba 22 kaya! how can the consumer keep up? show them nyau king. we can wait 2 years for quality music
Its not how long you spend your time in studio but how ur talented and knw wat to do at the right time i think its the right time to take music seriously and take it as a career b well connected!!!
kumalawi kudachuluka nsanje kwambiri mwayamba kale kumchitira mzanu nsanje,amene ukulimbana nayeyo sisaizi yako wamva iwe limbani?umafuna ukhale iweyo namba 1 munthu osatchukanso ngat iwe,kulembanso kumakuvuta ndiinu anthu aja amene mumathawira sukulu pa windo,kungoziwa kulemba pang’ono bac mwayamba kale kulembanyimbo zosamvekanso ngati izo,ndemkumat mungakhale namba 1.zankutu bac,mmalo moti mungonyadira kut mmalawi mzako wachita bwino koma bac kumpezera tizifukwa ting’onoting’ono ndimpake amalawi ambiri sakuchita bwino chifukwa chamsanje
I am In full support of Mwanache ngakhale enanu zikukuwawani koma mwangoti ndwii ngati akuchotsani dzino apa.Tiyeni tinene zoona ;Nyimbo ya Kang’wing’wi king imene ikuhita ma airwaves pano ndi iti?????I am baiting K10,000-00 mukandiuza.Pano nyimbo zimene tikumvera mu hoodumu kaya ndi trash kaya ndi beef koma at least they are on repeat ndi achina Mafo’ Babie yanga,Blacks tidzingocheza,Sonye,Tsika Msungwana izizizi musadzabwerenso next time kuti Malawi Music awards kaya ndi chani!!Better call it”Nyau King Music Awards” because we know he is automatically the winner come what!!!!
Money talks,Money rules,…go to school, make it big, get big money..long paper then do the exact songs u did 6 years ago, oh lastly bribe the judges, or let them fear ur name…. whatchu thought? That’s how the world works..
It depends.Mwina mzanu is heavily competitive pamene inu mukutulutsa trash.We r living in a competitive world and people are looking for quality not quantity.There is no creativity among many Malawian musicians and their videos are of very low quality.Pull up your socks and stop moaning like a baby ndi zichewa zako uyooozo even though im not a fan of Tay Grin.
Iwe kulongolola bwanji?naweso ingoyimba imodzi then ujambule Video,mesa amavota ndi Anthu kodi…