Ten Malawi police officers arrested for stealing
Police in Malawi’s central district of Salima have arrested ten police officers for allegedly stealing government equipment at a Green belt Initiative site in the district, police officials have confirmed.

National police spokesperson Rhoda Manjolo told a local radio on Tuesday that the officers who were guarding the site last month, allegedly went away with iron sheets and welding machine last month.
“Yes the officers have been arrested after authorities at the site lodged a complaint over the missing equipment,” she says declined to mention the names saying this would jeopardize ongoing investigations.
Statistics show that the arrest of the ten now brings to 16 the number of police officers arrested within a month on allegation of theft after four were arrested in Chitipa and two in Mangochi.
Low pay is no an issue be oz when applying for the job we are told the conditions and terms.ngati sumuyifuna umasiya
Ine ndiye sindimadalira za ma POLISI zanuzo, polisiwanga ndi YESU ,ndi agero ake basi, osati omanunkha khwema poyendawa,
Wow. I can’t believe this. How could law enforcers break the law.We can not blame much may be they earn peanuts. Government step up and solve the crisis. Punish them to make lesson for other law brokers
I’m sorry guyz ,use athief to cache a thief
Khondo nd anas nd anthu amwewa amene amabweka akuba mfut kut kumatbera manyumbam
unfair&unacceptable behaviour,law enforcers why?
Wa Police wina aliyense ndi wakuba,waziphuphu komanso wakupha dziko lonse lapansi.Kusagwidwa kokha ndi kumene kumawabisa maka kuti tsiku lawo limakhala lisanakwane
umphawi wathu amalawi pano nde wawonekela patali apolice abe,akuluakulu amboma abe, ampingo abe ngakhale mtsogoleli wa dziko amene abe nde athetse umphawi wathu ndindani? ngati dziko latilephela tingoligulitsa ku nearby country
SO WHO IS GOING TO PROTECT THE PUBLIC, SORRY POLICE
A police akumaba kwambiri ponamizira kugwira anthu omwa ma sachet, e.g a police apawenela ku blanyre, akagwira munthu bcoz of sachet akumusiya akawapasa k 2000
Comment:ints too much for u policemen mpakana malata?so who will securer our properties.
The issue here is not about salary. Who is satisfied with his/her salary? The more the increment the more the problems. Kuba ndi khalidwe la munthu osati mukumenazo. Kodi munthu akapezeka kuti wolakwa amamutani? Period!!!!!!
poor people fuc**k
Point of correction in Chitipa 5 not 4 so the total is 17.
Hahahahah welcome to the end of days…
we have a long way to go!Police steal in our country! Lawyers steal! why have we lost self pride where we work for what we get?
Amwenye at fault again?
If not amwenye, it is a Tumbuka at fault. See how the blame is on ‘low salary’ when it is them.
Apolisiwa ali pa mpikisano. Apolisi omwe amalondela akumati akawona anzawo a traffic akusitha magalimoto kumanga manyumba apamwamba nawonso olondelawa akufuna kumagula ma galimoto ndikumanga nyumba za pamwamba komanso kukhala moyo wa pamwamba ngati anzawo a traffic. Ndiye njira yoti nawonso apeze zonsezo angatani?? Njila yoyamba ndikumanga athu ngakhale osalakwa kapena kugwila anthu osawuka amene akuwoneka kuti sanasambe kapena oledzela mmabala ammakwalala ndikumanena kuti vakabu. Akatero amakuwuza kuti dzipulumutse ndi ka 5 pin. Njila ina ndikugwilizana ndi akuba powabweleka mfuti uniform ndi unyolo kuti akabele azagawane. Sinanga a traffic akuwalemelera anzawo mmaso iwo akuwona ndiye muli inu mungatani nonse mukugwila company imodzi maudindo ofanana kungosiyana ma department koma nzanuyo akulemela modabwitsa. Nawenso umaisova kuti nonse mufanane. Ndiye ngati mukufuna kugwila mbava mu polisi muyambe ndi atraffic amenewa ndiye akuba kwambili mu polisi. Komanso chopweteketsa mtima kwambiri ndichakuti atraffikiwa akumati akatibera ndalama pansewu akumakagula ma minbus awo. Ma minbus awowo akumapachila anayi anayi. Iwe kungoyerekeza yako kupachila 4# 4 akukugwila uwanyemele basi. Ine ndikupepha boma liwunikenso bwino malamulo ena apansewu chifukwa timilandu tinati tikungothandizila kuwalemeletsa akanganyawa.
Comment
kma dzko likutha et.
Asiyeni nawo azidwapo awona inu akuluaku aboma mukuba ndiye Iwo azingoyang’ana
kkkkklklkl phele kunowa mpaka kuphana
kkkkkk nkhani zinazi
Zonse zimene za Kamuzu Banda! Nyumba zawo! Zovala zawo! Ndodo zawo! Nsapato zawo! Ma office awo! Zakamuzu Bandaa!
hahahahahahah zoona amalawi!! nazoni achewa inu komaheheheh pa ntumbo pano
Ohh yesss…hahaha,welcum to malawi
Kikikikiki, tiyeni nazoni pa Malawi
galu ndi galu olo adulidwe mchira sangakhale mbuzi. amapita kupolice kukanamizira kugwira ntchito dzili mbava zoopsa.
Comment: Kodi a police mwalowa chiwewe? Nanga akuluakulu mukutinji ndi mchitidwe wakanganjawa? Choyambilira mudzawona kuti a police ali akatakwe munkhaniyi ndi amene akukhala muma location. At least 99% mwa mbavazi ndizimene zikukhala kunja kwa mpanda. Boma ganizirani nyumba zoti anthuwa onse adzikhala malo amodzi.
Madam Rhodah, you are beautiful indeed how are you then. I will visit your office today for congratulations ONLY.
Poverty among policemen is the root cause of all these thefts. The traffic police steal from road users. They mostly target notorious mini bus drivers.
Comment…..PETER, YOU BETTER RESIGN. YOU HAVE FAILED TO CONTROL THE SITUATION. THINGS ARE GOING OUT OF HAND. OUR SECURITY IS IN THE HANDS OF POLICE WHO ARE THIEVES THEMSELVES. PETER PLEASE RESIGN FOR THE GOODNESS OF MALAWIANS.
Comment umadya pomwe akumangilia mukuti atani wapolice pamene akulandila ndalama zochepa
La 40 lakwana,mumayenda mbali.
Anyanya a police aku Salima akufunika ma Transfer onse.Mahule awanyenge ulere ati kuti asawagwile vacab,kuba ndiye chisimu tifere kuti ndi a police?chonde chitanipo kanthu akubawa si anthu wamba ndi apolice omwewa.
not only Malawi even rich country upeza a police okuba okhaokha traffic ndiye eeh mbava . immigration mayo okuba kuti adinde passport like opita RSA R100 polowa zuwa amaba zingati ? weakness ndi bomalo and now for property to be safe not hire police but local people they are stupid even akakongola sabweza they think they are GOD
Apolice mukutichititsa manyazi. Mwaonjeza.Muziwapatsa chilango chokhwima.
Comment Zimenezo ndizomwe mumafunila kuti chipani cha DPP chipambane paja amapeleka ufulu kwa apolice ndiponso ndiomweo amawauza anthu kuti avotele chimanga lelo ndizo apolice akungoba ngati munthu wamba nanga pamenepa chitetezo chilipo?Tithanananu ndi mfumu yanuyo agalu okuba inu.
That’s why the MDF just welcome them with boots.
Wapolisi @ 22 you are a bastard. Whether you are a police officer yourself or your Papa or Mama nonse you are idiots. We have security in our houses because of our own measures poti these days kukada we are afraid of the same police kuti atithyolera manyumba. All Police officers stupid zanu. Pano MDF ikugwira amakala protecting nkhalango mukudandaula because inuyo mumapeza cholowa through amakala. Ziyambenso kuvala akabudula ziagalu zimenezi, anati zizibvala ma trouser ndani???
Shame. Wapolisi (a reader, comment No. 22) has just managed to tell the nation what many of us have been suspecting all along – that in Malawi, police officers are above the law. How come Wapolisi knows exactly what is going to happen to his fellow officers? He knows EXACTLY how the issue is going to be handled, and that at the end the arrested officers are simply going to be transferred elsewhere. How does he know this? Because these are the assurances they are given by their bosses as they go about stealing from people. They are assured of protection from above. How do you like that piece of revelation Mr. Inspector General? Wawululatu uyu! This raises enough interest in people like me to follow the issue closely to see if the whole MPS is indeed going to fulfill what Wapolisi has PREDICTED. Mr. IG, we are waiting and watching VERY VERY CLOSELY!
Ngati ndimavoti zikugwirizana. Kaya dpp inabera kaya ayi tiyeni tithandizane kutukula dzikoli
Comment malamulo agwire ntchito
Malawi is a God fearing nation and where are our christian values in working places? There are unbelievable cases of thefts and corruption involving very important people in Government that can even give instructions to officers to investigating a fraud case. very sad indeed.
Shame to u police!
Disgrace to the uniform
ife tilibepo zolankhula pamenepa. Akanaba anthu wamba nkhaniyi mukadayifufuza bwinobwino koma ma officers anzanu ngati amenewa kaya ndakayika.
kawalala aziba kawalala munzake
The problem is recruitment. They recruit there son and daughter and thats why stealing
No.10 Ezekiele Peter Ching’oma, kani ndinu osazindikira motero kapena ndinu mwana ongobadwa dzulo lomweri? ino ndinthawinso yomakamba za MCP???? Inu simukudziwa zomwe MCP inachita mudziko muno? Kapena ndinu alendo kuno? Becareful ndi congress yanu mukuifunayo. Pitani mukafunse akuluakulu akakuwuzani zakuipa kwa chipani chimenechi cha MCP
My poor malawi,this is the reason of not get enough from there duties ending in such situations
mwakula mwatha musova!
Its very had to comment on what u write bcoz sometimes u just print stories contrary to what happened. U seem not to get ur news from reliable resources.
Mbuzi imadya pomwe aimangilir a ndiye moyo wa pa malawi pano ,nanunso amene mwawa manga anzanu mudzaziona mukazakhala mmaluzi nsanje basi…….
Tinene kuti boma likulephera? Tinene kuti apolisi ngakuba? SHOOT TO KILL.
Can somebody advise me, kodi wa police wa traffic akatenga bribe ndiyende nayo bwanji nkhaniyo kuti ACB aidziwe. Agalu awa ndatopa nawo!
Ngati mukuba inu eni chitetezo kulibwanji ife?
muziona mwakula kale inu
timadyera mmenemo kaya musatimange. kuwabera kwambiri alimi ife apolice.
Give them enough money if u want this to stop, otherwise…….dont blame ’em.
Malawi police:are they law enforcers or a bunch o crime enforcers.Comment
Malawi police:are they law enforcers or a bunch of crime enforcers.How do u conduct the vetting. This is disgusting.Comment
Comment: Boma la Malawi lakhala ngati komboni ya anthu osokonekera. Chitetezo chikuchepa mpaka na apolisi kumababso eeee ati ateteze dziko tsopano ndani?
Very shame!!
wapolisi wakuba adziphedwa basi
Apolice ngati akuba nawoso agwira bwanji mbava chifukwa iwoso ndi mbava.Kodi ngati apolice akuchita zimenezo tiwakhulupirira bwanji?.Ifetu sitimadabwa kuona chigawenga chpopezeka ndi milandu ngati iyi; kuba poopyeza ndi mfuti,kupha anthu ndikuwa chotsa ziwalo ndikudikirira anthu panjira ndikuwalanda katundu,Ndikutulitsidwa mu cell zimakhala zinthu zodabwisa,mumakhala kuti ndinu anthu amodzi.Yehova akulangeni anthu osakhutisidwa ndi malipiro anu nonse.Zikoma kwa apolice onse amene simumaba chifukwa enanu ndi anthu opemphera mchowonadi.
Koma Zinaz Zanyanya Ndiyeno Amene Apeleke Chitetezo Ndindani Ngati Apolisi Omwewo Ndiamene Akutibela?
True criminals terrorising our society are these,thugs in cops uniform!
Shoot to kill them osamangopha ma civillian okha
Ndiambili kufufuzani enanso agwidwenso.mbamva osazinyengelela amangeni ngati mmene iwo amachitira wina akaba.
Shame!
police in our country are well paid.., it’s clearly seen by their living standards, most of them have cars, can afford to subscribe dstv, they have built mansions..
unless u tell me that most of them are stealing, only that they haven’t been caught yet.
Malawi at auto pilot!
UNYOLO WAO UMENE WA AMANGA. MWESO OYESERA ANZAKO NDI UMENE ADZAYESERENSO IWE. KHAU…..U!
Azimangidwa basi lamulo lizigwila ntchito
aonjezeleni saraly anthwa ikcepa thats why amaba
Dont take law and your hand apaseni belo ……..
Dont take law and your hand apaseni belo
Malawi watayika..ife tikufuna ntchito mapepala athu akungokhala,taonani zipanga a gang’aziwa,achule,asakunda..tikupita kut nd dzikoli kod?mwina salary yawo ikuchepa?apatseni loan bas abuluziwa..amipala ngat yot amametela grinder
Its not only them, go to Soche police in Blantyre one CID officer conive with robbers and its really difficult nowadays to catch robbers. His name is Gondwe. He is a nuissance. His fellow mates confess this. If your case is with Gondwe just know that you will cry.
This z bullshit,,mbava izi,,
You people take care loosing a life for u and leaving our families pamchere is not a joke learn to appreciate efforts from Malawi Police Service as well as GVT, think of these points 1- you live wth robbers, thugs,thieves, defilers,rapers in our communities and we know them but we never communicate to police about them ,who is failing police then, since we r part of police let’s take part in combarting crime instead of pushing blames on police officers. In such a case we shall develop
As you can get it clearly protecting life and property, means their life first then yours if you are Patriotic but if ur unpatriotic then its a game of tit-for-tat, coz if we. Kill them you say shoot to kill. What do. You want us to do. We need not to oversacrifice ourserves. Since police is a service now not a force and ur part of it
Manjolo mokupepha kwidzinga ose usanyengelele amenewa ndi mbutuma ndinthu.
ALL ROAD BLOCK IS BIG CORRUPTION REMOVE ALL BRING NEWONE
lack of professionalism… shame!
Apolisi, ndimaloya ndiamene anathandiza DPP kuti iwine. Pamene apolisi amathandiza kuba mavoti mumasenta ovotera, maloya anali kalikiliki kukonza zakuthi kuti mpaka Pita adutse basi. Cholinga chinali choti adyenalo bomali. Ndechifukwa chake zikuchitika izi. Ndende za m’Malawi kudzadza ndi apolisi ndi maloya.
Comment: kaya zanu izo
Ma-kape inu muli safe in ua homes bcox of Police and ua bixy tokin shit hea 4getn dat diz royal offices risk thea dear lives jux 2 protect morons lyk u! Ma guyx omwe amangidwa ku salimawa atuluka pompano n tha gvt shal pay them huge compasationx cox palibe umboni woti anaba n a casefile ya theft xingaxegulidwe…anthuwa amangidwa bcox anabexa pamalo xo they wil only b dealt wth internaly ndipo angopaxidwa ma transfa ax a punshmnt..! Dnt b brainwashd by diz negative media..u nid 2 av a thnkn head by analyxin thngx logically mwamva inu ma civilian?
We are safe coz sitidutsa komwe kuli abulutuwa, amangoombera anthu osalakwa. Taziona ku Mchinji kuno mpaka kumaombera alendo ma ofesala aku Zambia. We r safe with G4S not apolisi aku malawi omango khalira kupempha pa nsewu.
@ wapolis malembedwe aumve awa {please change} wakopera udyo
brainless police officer. i assume u havent gone far with ur training and ethical codes of conduct. no wonder u r stil constable at that age. kumanyadira anzako atapanga zopusa zoona? idiot! kuzolowera kudyetsa agalu basi!
plz, things r going out of hand with these serious allegations of these police monster. Too much thieves here in Kasungu, armed robberies, robbery with violence, etc. But eversince, these criminals have never been identified, it’s always been transpired that police officers are involved. We can’t rule out these serious allegations, let the higher authorities interveneand investigate about this. Filling stations have been heavily hit in Kasungu but their investigations are in limbo just because they are accessories to.
MBAVA ZONSEZI NDI A POLICE WOMWEWA
AMANAMIZIRA MA VENDOR !!
khani sindalama ayi athuwa ndi akuba basi
Comment shameful
Low wages is no excuse. Mbava ndi mbava.Who forced them to join Police??Where are they from???
its not the issue of wages these chiefs period. you expect them to be receiving millions after spending six months in training yet others they spend six yrs training at college of medicine yet they are also receiving peanuts
No trust at all
Asanamizire kuti amapatsidwa ndalama yochepa pamwezi. Kodi pamene ankafunsira ntchitoyo sankaziwa kuti ndala yamalipiro ndiyochepa? Nanga panopa ndalamayo yapamwezi yaonjezekera. Anthu amenewa ndi akuba basi. Osawamvera chisoni. Ice anthu ogwira ntchito m’boma tonse timalandira yochepa yomweyo koma sitiba kuti tiwonjezere. Amene amaba ndi anthu olandira ndalama zambiri mucashgate
Wina akhala chilinda wonama mu court. Police are useless
A police ndi mbava koopsa timakuuzani. Anthu omvetsa chisoni. Mmalo moteteza akuyamba ndiwo kuba. Zitsiru za anthu. Zimangokhalira ma sachet basi ndikuliza mikonono muma office. Afisi achabechabe
Their wages are pathetic. They wanted to make the ends meet
Police Officers under MCP can not do this
Security tightenz
The laws in the country are sick hence the pilfering business worst the Law enforcers. Abuse of democracy.
The law must take its course.They should be prosecuted accordingly.
Slim wages,,,,giv dem enough money
Mbava ndi mbava mukuzibisilanji?kasambala anaba munavomera kuti mwamumanga what about okuba malata achuleni tiwaziwe.APOLISI 10 asalapo angati pastation po?ili ndiboza lenileni amalondela bwanji onsewo pa sabata imodzi
Thts Malawian’s…Police…
MAlawi @ 51
apatsidwe chilango chokhwima,apolisi kubanso ndiye ateteza dziko ndi ndani,ook kenaka mudzava kuti WA polisi wawoychedwa ataba sure musadzadabwe.
Umphawi