Bushiri watulukira! Agawa chimanga kwa anthu opitilira 1 million, chokwana K14 billion

Mtsogoleri wa  mpingo wa Enlightened Christian Gathering International Prophet Shepherd Bushiri walengeza kuti ayambiranso kugawa chakudya kwa anthu opitilira 1 miliyoni omwe akhudzidwa ndi njala mdziko muno.

Malinga ndi mneneri Bushiri, ndondomekoyi ipulumutsa Amalawi mamiliyoni ambiri omwe akhudzidwa ndi njala pazifukwa zosiyanasiyana monga Cyclone Freddy.

Bushiri wapempha mabungwe akuluakulu aboma ndi anthu onse kuti awonetsetse kuti zinthuzi zomwe mkuphatikiza mpunga komanso ndalama zifikire anthu onse okhudzidwa.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Sharing is caring!

Follow us in Twitter
Read previous post:
Chakwera sees Malawi food secured this year through redesigned AIP, Neef loans, mega farms synergy

With the redesigned Agricultural Input Programme (AIP), provision of loans to medium and large-scale farmers and rolling out of mega...

Close