Chipani cha DPP chichenjeza boma: “Osapanga bajeti yokopa anthu pa zisankho, thesani njala, konzani chuma.”

Chipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) chachenjeza boma kuti lisakhazikitse ndondomeko ya chuma cha chaka cha 2024 mpaka 2025 yomwe cholinga chake ndi kukopa anthu pomwe dziko lino likukonzekera zisankho.

Navicha: 

Chenjezoli likubwera pomwe nduna ya zachuma, Simplex Chithyola Banda, akuyembekezeka kupereka ndondomeko ya ya chuma ya 2024/2025 masana ano.

Polankhula ndi MIJ Online Mary Navicha, mtsogoleri wa DPP m’nyumba ya malamulo wanenetsa za kufunika kwakuti boma lithane ndi vuto la njala ndi zachuma lomwe Amalawi akukumana nalo mu ndondomeko ya chumayi.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Sharing is caring!

Follow us in Twitter
Read previous post:
CCEDI raps Chakwera: Says Malawi leader lied that passport system has been hacked

Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) has come in strong against President Lazarus Chakwera saying the Malawi leader...

Close