Lilongwe woman arrested for Indian Hemp
Malawi Police are keeping in custody a 31-year-old Lilongwe-based woman Martha Kawale for allegedly being found in possession of Indian hemp.

Kawale was arrested at Kaphili residential area in the capital according to Lilongwe Police Public Relation Officer, Kingsley Dandaula confirmed the arrest.
Dandaula said Kawale hails from Tchoyo Village, Traditional Authority Kalumba in Lilongwe District.
“Police got a tip off from people surrounding the area that the suspect was keeping Indian hemp in her house intended for business,” said Dandaula.
He said: “A search was conducted in the house of the suspect and in the process, four bags were found in one of the rooms.”
He said the four bags of Indian hemp would be sent to Chitedze Research Station for examination and that the suspect would appear in court to answer the charge of being found in possession of Indian hemp.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
Robbers are working everyday smoothly inu mulipo,osawagwira mukalimbana ndi munthu ofuna nchere wake pakhomo.Bwanji osamanga mbavaz ndi uyu nzanu waku Blantyre amapereka mfuti kwa mbava zobera?Zopusa basi ka Police kopanda manyaz,Msiyen nzimayi uyu alibe chifukwa!si cashgate iyi kapena Nacgate.Ndineyo waku chigodi ngati mwakhudzidwa bwerani ndikunyenyen phuno zanuzo,mulibe nzeru futsek.
Nzako zimenezo, mzako wogulisa chamba wagwidwaa, wasala ndi iwe
limbanani ndi akuba ndi mfutiwa osati uyu ayi
kod chikapita ku chitedzeko aftr kuchiyeza m’matani nacho?ngati m’maotcha dats bullshit..its better kumpasa munthu akaguritse apeze dollar ya sxul feez…
my food kkkkkkkkkkkoooohhhhhhooo
achina Leonard Kalonga akungpyenda mwaufulu kudya makobidi a cashgate inu mukulimbana ndi mzimayi! Robbers are just killing you and terrorising homes there is nothing you are doing. Musiyeni munthu mumati akakudyerani kuti. Komanso amene mumamuneneza nzanu ndinu anthu osowa chochita. fotseki nonse
Legalise seimier in Malawi.
Ma jealous basi. Mzanu akakudyerani pa khomo pa mbuyanu? Mmalo moti muzichita zanu mwafatsa kukanenera anzanu. BOLA KUGULITSA CHAMBA KUSIYANA NDI CASHGATE …
Previous culprits have being handed charges of chamba possession wthout a licence. Who does the issuing of licence? I want to have one, ndikuopa, ndingadzavutike msika ndikadzakolola. Otherwse I ndachilima zedi, and I ddnt kno that it is drought resistant crop. Scientists at Chitedze, ths is a researchable area if u ddnt kno.
Ndi samba osati chamba. Bwanji kodi. Mai wanzeru uyooo. Osati zomapha zamalungazi
Martha Kawale is a thief she swindled me some cash in pretext that she is stranded has a patient going to KCH and has no fuel in her car. I lent her my money and she disappeared! Wages of sin!
Pepani.
Muzikwizinga Oba Misonkho Ya Anthu,leave The Woman Alone,more Over Analetsa Kulima Ndi Kuglitsa Chamba Ndi Asamunda And Iwowo Ankagulitsa Okha Kudyera Masuku Amalawi!Palibe Cholakwika Ndi Chamba’koma Ma Minister Ndi Mabwana Akuba Mmaoficemo.
Other pipo doing big stuff than this …leave her
Tamusiyan Munthu Wa Mzimayiyu Mulimbane Ndi Akwatiwa Ndi Dzigawenga Zapolice Zobweleketsa Mfuti Zaboma
mwana wa abusa kodi?m’bale wake wa ujeni ndi ujeni?
she’s just struggling for a living, after these are weeds, sanatchole mnyumba mwamunthu. please set her free and resume her business!
these cases of indian hemp achuluka these days
Mpatseni chamba chake zitsilu inu, anthu akuchisuta mtauniwa simmawagwila bwanji? Mbanva apolice nonse siinu mukutchola ma Bank mukukalimbana ndichamba? Mwina amalipilila Fees ana ake kudzela mu Bussnes yomweyo kapena mukufuna mumukwele mzimayiyu?
Koma nde. Umasungira kowawatu geni koma imeneyi kusiyana ndikupanga u hule nanu apolise mukukanika ku gwira anaba ndalama za boma aja bwa
Kutakatatu kulibe kuti uwu ndi mtundu wanji wa business bola ndalama .Titakate amai zaka zake ndi zino.
Grades get me high.
So high that I can meditate….!
Chorus
Dreams of brighter days aha! Aha! Aaha!
Highest grades we blaze aha aaha!
Giving thanks, giving thanks and praise……
Azimayi a MCP! Wina ndi uja wa short tsitsi uja! Kaya samasuta kayaaaa!
No case here!
Zikatha m’mbewa anona ndi swiswili. Mukuziwa kale kuti anthuwa koma kugwila munthu wamba pamene mbava za jekete zikuswa ma Bank.Big up mum
I’ve never heard of police disposing off this stuff, mumatani nacho? Ambiri amagulitsa ndi ma agent a apolisinu ndipo simuwa manga. Its time we should be handing over to pharmacy and poisons board for disposal of this dangerous substance. Apolisiwa akungodzi sutila mix kupatsa ma agent awo nkugulitsa thukuta la enali!
kodi iyeyo waba?muzigwila mbava zikukuphanizi.
Pepani mama akugwilani ndi mgodi
Nanga atani maiyo pakuti dzikolo lanunkha musiyeni maiyo azipitiliza geni yakey.Mukuleka kugwila aja adaba ku Bank aja mwasanga mukukachita changu pamaiu tikuonani kaweluzidwe kanu.
Apolice koma zimenezi basi,anthu akuba ndalama ,kuphana koma ine buzy kugwira wa chamba kkk
AZIMAYI AZIMAYI AZIMAYI PA NYAZALANDE !!
MWINATU NDI MFUTSO TIMVE KAYE ZOTSATIRA
Palibe khani apa, fotseki