Phungu wa DPP a Suleman akufuna mkulu wa Immigration atule pansi udindo

Phungu wa nyumba ya malamulo wa Blantyre South East  Sameer Suleman wati m’kulu wa Nthambi yoona za anthu otuluka ndi kulowa m’dziko muno (immigration) atule pansi udindo kamba koti palibe chomwe akuchita ndipo wakalamba.

A Suleman ati nzokhumudwitsa kuti mpaka pano ziphaso zoyendera sizikupangidwa zomwe zikusokoneza ntchito za a  Malawi ambiri.

Iwo ati izi zikuchitika pomwe boma la Tonse likutumiza a chinyamata kupita Ku Israel, zomwe ati apita bwanji opanda ziphaso.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Sharing is caring!

Follow us in Twitter
Read previous post:
Chisale threatened me, says DPP: “Angry people can be dangerous and are difficult to handle.”

Director of Public Prosecution (DPP), Masauko Chamkakala has testified in Court that Norman Chisale threatened him through a letter which...

Close