21 Malawi army soldiers face military court over misconduct in DRC
Some 21 Malawi Defense Force (MDF) soldiers and one officer start appearing a military court marshal Thursday following the killing of six Malawian troops by rebels in Democratic Republic of Congo (DRC) last year.
Two soldiers are still missing.
MDF spokesperson Paul Chiphwanya confirmed the trial of the soldiers but he declined to give details, saying it is “an exclusive matter.”
High Court registrar Agnes Patemba said Judge Chifundo Kachale has been appointed advocate judge over the matter.
The soldiers are accused of losing weapons and abandoning their posts. They face misconduct charges.
At least 13 soldiers are answering the charge of losing official weapons whilst eight are answering the charge of abandoning their posts.
The charge of aiding an enemy has been withdrawn.
Immediately after the incident, the MDF recalled the 21 soldiers who were on UN mission.
Defence counsel for 18 of the soldiers, Ralph Mhone, also confirmed the trial which is expected to start this Thursday.
Malawi isiye kulimbirana nyanja ndi TANZANIA chifukwa DZIKO la TANZANIA lili ndi ASILIKALI pomwe ife tilibe.Choncho tingaonongetse ndi kuphetsa anthu osalakwa mziko muno.Kumangodya nyemba ku barracks ndi kuononga ndalama zaboma for nothing ku nkhondo ndi kumathawa, inu mungasiye mifuti ndikumakaonera mpira kuli kuthawa??.ASILIKALI Aukape.
Dziko la malawi lilibe asilikali, adzatipha kuno asilikali amaiko ena poti ku malawi kulibe asilikali.Kunkhondo mpakana kusiya zida ndikumakaonera mpira zoona agalu inu?.
Vuto ndilakuti kutumiza ku mission chifukwa choti pali ndalama pamachuluka kukondela. Amapita kumeneku ndi anthu oti usilikari weniweni mulibemo koma ziphuphu zopasa mabwana. Muzawona kuti ma khuki, ana ongolowa kumene ngati ali ana amabwana kapena azibale awo. Ndi ena amene sangakwanise ntchito yaku DRC ndi amene amasankhidwa chifukwa cha ziphuphu. Izi sizodabwisa.
Very disgusting and embarrassing news. Apa the whole world knows kuti ma soldiers aku Malawi amathawa nkhondo mpaka kusiya mfuti. Mukalembere ntchito yakolopa mzikumba popeza kutchire kwakulakani. Mumangodziwa kuvina perete basi
Mbuzi za anthu…Ndendimuone wina Ali fwefwe Ku ViBES lero..Ntchito mahule ndi kuba mafuta agalimoto basi. Nanga TATa iziyendera neutral…MT Zomba airbase ndiyamba kukutchulani..
Timadabwatu ife akamati mdf is a disciplined army kuti koma akunamiza ndani kwenikweni. Kudzikwata ndi chala. Idzi ndi dzidakwa basi mowa wakenso wopemphera makani
No comment.
Abweze mfuti zomwe anasowetsazo tikuzifuna. Zoona msilikali kuthawa ngati galu okuba ndiwo mu mphika kwinaku atapanira mchira. Shaaaaa.
This looks like a grave breech of discipline, if not actual cowardice. The MDF are so ‘brave’ when dealing with their own citizens at home in Malawi, but appear to lack courage when facing a real enemy.
Sopano amathawa chani mayesa analumbira ndipo timawalipira ma Allowances a misonkhoyathu on top of their UN dues zachibwana eti mwatipangisa manyazi zitsiru za ma soldiers anzanu analolera kutaya miyoyo yawo kuzipereka koma inu mumaganizira kunyenga achakazanu kunoko ku malawi alaaaaaaa mulandire displine basi komaso nanu ma coporal aku MDF muli ndi vuto ndi ziphuphu mumatumiza anthu opanda siliyasi pa ntchito anthu ozipereka mumawasiya coz simudyanawo bwino osawalemba ntchito kumalemba mbuzi zawanthu nanga look now look zachibwanatu izi aaaaaaa